ZIKUCHITIKA POMPANO JOSEPHY MKASA WAIMBA NYIMBO IYI PAMASO PA A CHAKWERA KU CONVENTION YA MCP

70,623
0
2024-08-08に共有

コメント (21)
  • Mkasa amadziwa kutembenuza chikwangwani! Change goal! Beautiful song, beautiful composition, wise timing!
  • Koma ndalama anakonza ndithu zomwe akuchemererazo za ziiii aaaaah
  • yomweyoo ,,, wawulesi asadyee ,,, amene salimbikira pa yekha nde zimuwawa ,, dikira chakwera azakulimira ku Munda kwako
  • Nkasatu ndi oyimba ali ndi ufulu opanga kuti zake zimuthekele nane kwathu ndi ku alomweko koma ndikugwilizana ndi mfundo za chakwela tonse ndife amalawi osayang'anila mitunndu
  • Nkasa is an artist, he can be hired to go and entertain people at any function. Musamunyoze chifukwa choti wayimba nyimbo ku msonkhano wa chipani chomwe mwina simugwirizana nacho. Next time he can be called to entertain people ku Convention ya UTM, DPP, UDF, AFORD or any other party. So izi nzabhobhoo. 🇲🇼🇲🇼🇲🇼
  • Mkasa samakwera yakuphwa uyu amaonera patali mita akutanthauza china chake chachikulu mawu akulu akoma a kagonera.
  • Guys when u are poor u do anything to make happy they Richie people 😂
  • Nyimbo ikukoma iyi,, Ife tikunva kukoma Enawo akunva kuwawa eish 🎉🎉🎉🎉
  • The song deserves a video, nice one in that matter, with all the infrastructures included.
  • Ine ndingowerenga ma comment basi 😝🤪🤪🤣🤣🤣🙌
  • Chipolopolo kumalawi pamaimbidwe mcp wooooyeeee 🔥🔥🔥🔥🔥🔥 big up
  • Kuyankhula kwa Anthu ANDALEE amati “there’s no permanent enemy in politics “. Nde J. Mkasa adzituwa milomo pomwe ku MCP vinyo alipo.